Trudga-D Mw malawi songs

Trudga-D Mw

1 follower

Biography

Ndine woyimba wa nyimbo za secular wochokera ku Zomba, Malawi. Ndimalemba ndi kuyimba nyimbo zomwe zimafotokoza moyo wa tsiku ndi tsiku. Cholinga changa ndi kufikitsa uthenga wanga kwa anthu ambiri komanso kuwasangalatsa kudzera mu nyimbo zanga.

Popular Tracks

Explore more Malawi music

Browse more Malawian artists , the latest new songs, or what's trending right now .

MalawiSongs v2.1.0