

J Beater
0 followers
Biography
Trap artist from Ntchisi,J Beater ndi trap/hip-hop artist waku Malawi yemwe amapanga nyimbo zokhudza moyo, chikondi, kusweka mtima, komanso zolimbikitsa. Amagwiritsa ntchito Chichewa ndi English kuti afikire anthu ambiri komanso kusonyeza komwe akuchokera. Sound yake ndi emotional trap yokhudzidwa ndi ma vibe amakono, ndipo nyimbo zake zimanyamula uthenga weniweni wa moyo wa tsiku ndi tsiku. Cholinga chake ndi kuyimirira Malawi pa scene ya nyimbo zapadziko lonse.
Artist hasn't uploaded any music.
Discover Similar
Explore more Malawi music
Browse more Malawian artists , the latest new songs, or what's trending right now .
MalawiSongs v2.1.0