Ezzie Mw malawi songs

Ezzie Mw

0 followers

Biography

Ezzie Mw , Dzina Wezzie Ndhlovu, ndimachokera ku Mzimba ndipo pano ndikukhala ku Lilongwe. Ndine artist wa Amapiano yemwe akndikuyimba nyimbo zokhala ndi mauthenga amphamvu olimbikitsa komaso kubwelesa chiyembekezo pa moyo. Ndinayamba kuyimba mu 2019 ndi cholinga chofalitsa uthenga womwe ungathe kulimbikitsa ndi kusintha miyoyo ya anthu. Masomphenya anga ndi kuona nyimbo zanga zikufikira kudziko lonse lapansi, Nyimbo zanga zodziwika kwambiri ndi Mwamzeru ndi Addicted.

Artist hasn't uploaded any music.

Explore more Malawi music

Browse more Malawian artists , the latest new songs, or what's trending right now .

MalawiSongs v2.1.0